Malamulo

Malamulo

Malamulo

Tsiku lothera zinakonzedwapo: January 24,2018

Conde werengani malamulo awa ("Mau", ndi "malamulo") modekha m'tima musanayambe kusewenzetsa keyala https://betblocker.org/ ndi cosewenzera ca a BetBlocker ca pa pafoni yotsogoleredwa ndi a BetBlocker ("Ife").

Kusegula ndi kusewenzetsa kwanu kwa cosewenzera cathu, kuona cabe pa inu kuvomera malamulo awa. Awa malamulo akhuza onse alendo,osewenzetsa cosewenzera cathu.

Posegula kapena kusewenzetsa cosewenzera cathu citanthauza kuti mwavomela kulondoza malamulo awa. Ngati simuvomera mbali iliyonse ya malamulo awa, simungasewenzetse zosewenzetsa.


 

Ufulu wa umwini cinthu kusewenetsa nzeru

Cosewenzera ndi zonse zam'kati, mwamene cinapangidwira ndi mwamene cisewenzera zizakhalabe katundu ya a BetBlocker ndi amene awapasa ulamuliro osewenza. Cosewenzera citetezedwa ndi ufulu oletsa kukopa (copyright), ndi ufulu odziwira za malonda (trademark) ndi malamulo ena aku United Kingdon ndi maiko ena. Kadziwidwe kathu mu zamalonda simungazisewenzetse mu njira ina ndi malonda kopanda ufulu olembedwe kucoka kwa a BetBlocker.



 

Njira zina zosewenzera m'mphepo

Cosewenzera cathu zingakhale ndi njira zopita ku zosewenzera zina zimene sizilamulilidwa ndi a BetBlocker.

A BetBlocker alibe ulamuliro ndiponso sazakhuzidwa ndi zimene zili m'kati, zosewenzera zina kapena mwamene zinapangidwira. Ndipo mwavomera kuti a BetBlocker sazakhuzidwa paiwo okha kapena kupyolera mwa ena mu zoonongeka kapena kusowa kwa zinthu kumene kungacoke, kupitira, kapena kusewenzetsa zosewenzera zina kapena kusegula masamba ena.

Tikucenjezani mwamphamvu kuti muwerenge ndi kulondoza malamulo yamene yateteza zosewenzera za ena kapena mu zosewenzera mwina m'mene mulowa.



 

Kulemekeza ndi kuteteza

Muvomera kuteteza, kulemekeza ndi kusapasa mulandu a BetBlocker osewenzetsa ndi owapasa cilorezo cosewenza, anyancito ao, ndi ogwira nao nchito ena onse kulipilidwa poononga kapena, kusowetsa zinthu,(kuonjezera komanso kusalekezera pa kulipira ondiimililira pa mulandu) imene ibwera chifukwa a)cakusewenzetsa kwanu ndi kupeza cosewenzera kapena kuphwanya malamulo awa.




 

Polekedzera kutengako mbali

Kulibe mu njira ina iliyonse pamene a BetBLocker akulu anchito, anyancito, osewenza nao nchito, otumikira, ofalitsa adzakhuzidwa kapena kupatsidwa mulandu chifukwa ca kusaphindula, kusewenzetsa, kucita zinthu mwacifundo kapena kusaphindula kwina kulikonse kucokera mu (i) Kasewenzetsedwe kapena kukanga kwanu kusegula kapena kusewenzetsa cosewenzera (ii) zimene eniake acisulo zina acita; (iii) ili zonse zimene mudzapeza mu zisulo ndi (iv) kusewenzetsa/kukhala ndi cisulo kopanda chilorezo, kusewenzetsa kapena kusintha katumidwe ka zimene muli nazo, ngakhale kuti pali chipangano, kusasamala kapena zili zonse zokhuzana ndi lamulo, kapena tidziwa kapena sitidziwa pa ici, kapenanso tadziwitsidwa pa coonongeka.




 

Kudzimasula mu mulandu

Kasewenzesedwe kanu ka cosewenzera cathu ndi kodzifunira nokha. Chisulo cathu cipatsidwa kulingana ndi mwamene "cilili" ndiponso "ngati capezeka". itilonjedza coletsa cili conse copitilira pa mwamene chisulo cilili, taeni ake kapena kupitira mwa ena, kufika ndi kuyangana pa coletsa cimene sicili poyera ku zinchito, cimene cigulitsidwa kulingana ndi mwamene ciyenera kusewenzera kuopa kuletsedwa mocisewenzetsera.

A BetBlocker, makampane ao ena ang'ono-ang'ono, amene agwira nao nchito ndi amene amawapasa mphamvu zosewenza, salonjedza kuti; a) Chisulo cidzasewenza kopanda bvuto ndiponso kuti nthawi zonse cizikhala bwino; b) mabvuto onse adziwakonza; c) chisulo cilibe tidoyo kapena cili conse cingabweretse bvuto; kapena; d) kasewenzetsedwe kanu ka chisulo kudzakhala mwamene mufunira.




 

Zocotsamo

Kusacotsapo zilizonse pa tanthauzo ya zimene zili pamwambapa,kapena lamulo iliyonse, a Betbrocker sakhuzidwa mu njira iliyonse pa zobvuta zimene udzapitamo kapena wina ali yense kulingana ndi kasewenzetsedwe kanu ka chisulo cathu ndi kuononga phangano, kudula phangano kapena kuphwanya malamulo, kapena kupwetekedwa kwa munthu, kusowetsa kwa zina, malonda, misika, zosunga, malipiro, zophindula, kusewenzetsa, kupanga kapena ubwino umene ulipo kapena zoyembekezereka zokhuzana ndi zacuma( ngakhale mu phangano, kapena kupwetekedwa kwa munthu, kukhala ndi m'landu kapena lamulo ili yonse) ngakhale kungakhale kusasamala, kapena kusonyeza kuli konse( kuonjedzera kusasamala kwakukulu) kwa a Betbrocker kapena munthu wina ali yense asewenza ndi a BetBlocker, ngakhale kuti a BetBlocker adziwa zabwino zingatulukemo.




 

Lamulo imene ilamulira

Awa malamulo yadzatanthauzilidwa kulingana ndi malamulo yaku England ndi Wales, kopanda kuika nzeru pa bvuto yobwera chifukwa ca malamulo anaperekedwa.

Kukangika kwathu kosewenzetsa malamulo sikudzatanthauza kucotsapo kwa ufulu. Ngati kuti lamulo ili yonse ilibe mphamvu pa maso ya khoti, malamulo ena adzakhalabe ndi mphamvu. Awa malamulo akhala phangano pakati pathu kulingana ndi kasewenzedwe kathu ndipo phangonoli ipitilira mapangano ena ali onse analipo pakati pathu kulingana ndi kasewenzedwe.

Kuyamba kusewenzetsa
Ngati mwayamba kusewenzetsa chisulo ca BetBlocker ndiko kuti muvomera kuti mwawerenga, kumvetsetsa ndi kudziwa kuti cosewenzera ici cidzakuletsani kukhala ndi zosewenzera zina za njuga ya pa mphepo. Muvomeranso kuti simungacotse cosewenzera ici pa nthawi yovomerezedwa. Ndiponso kuti anyanchito athu azikuthandizani kucotsa tidoyo ta ici cosewenzera nthawi zonse pamene angakwanitse, ndipo sadzakuthandizani kucotsa cosewenzera ici.




 

Zosintha

Tili nayo mphamvu, kulingana ndi mwamene tifunira kusintha maphangano awa nthawi ina ili yonse. Ngati zosintha zifunikira, tidzayesa kukudziwitsani masiku makumi atatu zisanacitike. Camene cidzapangitsa kusintha kwa malamulo ndi kufuna kwathu.

Popitiliza kukhala ndi kusewenzetsa cosewenzera cathu pambuyo ya kusintha malamulo, citanthauza kuti mwavomera kukhala omangidwa ndi malamulo ya tsopano. Ngati simuvomera malamulo ya tsopano, muyenera kuleka kusewenzetsa cosewenzera cathu.



 

Malamulo yoletsa

Conde, onani ku malamulo athu ya pa zoletsedwa. Muvomera kuti izi ndi mbali ya malamulo awa. Muyenera kuwerenga malamulo athu musanayambe kusewenzetsa cosewenzera cathu.


 

Kuyamba kusewenzetsa

Ngati mwayamba kusewenzetsa chisulo ca BetBlocker ndiko kuti muvomera kuti mwawerenga, kumvetsetsa ndi kudziwa kuti cosewenzera ici cidzakuletsani kukhala ndi zosewenzera zina za njuga ya pa mphepo. Mwavomera kuti simungacotse cosewenzera ici pa nthawi yovomerezedwa. Ndiponso kuti anyanchito athu azikuthandizani kucotsa tidoyo ta ici cosewenzera nthawi zonse pamene angakwanitse, ndipo sadzakuthandizani kucotsa cosewenzera ici.


 

Kambani ndi ife

Ngati muli ndi mafunso pa malamulo awa, conde, kambani ndi ife kusewenzetsa [email protected].